Sei sulla pagina 1di 6

MTIMA WOYERA CATHOLIC CHARISTIMATIC RENEWAL

ENTRANCE HYM 1. NDINASANGALALA 1. Ndinasangalala pamene ananena kuti tiye ku nyumba ya Atate 2. Ndinalulutira 3. Ndinavinavina 4. Ndinakondwerera Chorus: Tiye kunyumba ya Tate,tiye kunyumba ya Tate 2. NYUMBA MWA ATATE NDI WANGA 1 Mnyumba mwa Atate ndi mwanga,mnyumba mwa Atate ndi mwanga. 2 Mnyumba mwa Tate ndidzayimba,mnyumba mwa Tate ndidzayimba. 3 Mnyumba mwa Atate ndidzakondwa. 4 Mnyumba mwa Atate ndidzavina.. 5 Mnyumba mwa Atate ndidzakondwa..

Extend a Welcome - to regular ,occasional and especially new members

3. NDAIFUNAFUNA NKHOSA YOTAYIKA 1. Ndaifunafuna nkhosa yotaika, I bwerere.(2x) Chorus: Ibwerere ibwerere (2x) Oh yasowa, ibwerere.(2x) 2. Ndawafunafuna abambo otaika,abwerere. 3. Ndawafunafuna amai otaika,abwerere. 4. Ana..AsungwanaAnyamata 4. KATUNDU WA MUMTIMA 1. Katundu wa mumtima,tula tula. Walemela ,tula tula,kapatse Yesu,tula tula 2. Machimo a mumtima. 3. Nkhawa za mumtima 4. Zowawa za mumtima. 5. Maganizo a mumtima

Opening prayer................. CONFESSION 1. NDIFUNA MAGAZI AMBUYE 1. Ndifuna magazi a Mbuye ,anditsuke machismo. Ndifuna magazi a Mbuye ,anditsuke machismo.

Chorus: Ndifuna,ndifuna,ndifuna magazi,Ambuye !! (2x) Ndifuna magazi a Mbuye,anditsuke machimo !(2x) 2. Ambuye thandidzeni,ndiulule machismo. Ambuye thandidzeni, ndiulule machismo. Chorus PRAISE 1. PAULO NDI SILA 1. Paulo ndi Sila anapemphera (2x) Zitseko za ndende zinatsekeka (2x) Chorus: Moyo wanga moyo wanga moyo wanga sangalala (2x) Paulo ndi Sila anapemphera Zitseko za ndende zinatsekeka. 2. Ukafuna kuyimba ,uyimbe mwa Yesu (4x) 3. Ukafuna kuyenda,uyenda mwa Yesu (4) 4. Ukafuna kukonda, ukondwe mwa Yesu (4x) 2. CHIKONDI CHA YESU 1. Chikondi cha Yesu ndi chopambana zedi, Chikondi cha Yesu ndichopambana. (2x) Chorus: Taonani) Iye anatifera pa mtanda taonani) chifukwa cha Ife (taonani) Iye anatifera pamtanda. Chikondi cha Yesu ndi chopambana 2. Magazi a Yesu ngopambana zedi, Magazi a Yesu ngopambana (2x) 3. TITAMANDE YAHWE HOSANA 1. Titamande Yahwe Hosanna Alleluai!Titamande Yahwe Hosanna (2x) EEE Hosanna!!EEE Hosanna titamande Yahwe Hosana 4. NDIDZATAMANDA OH YAHWE 1. Ndidzatamanda Oh Yahwe,Masiku onse amoyo wanga Moyo wanga,moyo wanga (4x) masiku amoyo wanga 2. Ndidzayimbira Oh Yahwe 3. Ndidzathokoza Oh Yahwe 4. Ndidzagwadira Oh Yahwe 5. ZOMWE ANACHITA ELIYA Zomwe anachita Eliya (2x) Anabeula satana (2x) Chorus : Beula Beula Satana (4x)

Ngati mufuna mukalowe (2x) muyambe mwabeula Satana.(2x)

6. AMBUYE AKUKONDA 1. Ambuye akukonda,Ambuye akukonda,Ambuye akukonda! Alleluai 2. Ambuye andikonda 3. Ambuke atikonda 7. TILI KUYENDA 1. Tilikuyenda mkwala kwa Mbuye,Alleluia (4x) 2. Tilikuyimba mkwala kwa Mbuye 3. Tili kukhala mkuwala kwa Mbuye
4. Tilikuvina mkwala kwa Mbuye

WORSHIP 1. NDINUTU OLEMEKEZEKA Ndinutu Olemekezeka,AAmbuye ndinutu opambana nthawi zonse 1. Ndikachimwa 2. Ndikadwala 3. Ndikatopa
2.

TIKUTAMANDANI !AMBUYE Tikutamandani Ambuye mwayeretsa moyo wanga Moyo wanga Ambuye mwandiyeretsa Ambuye mwayeretsa moyo wanga

1. Tikupembedzani 2. Tikuyimbirani 3. Tikuthokozani 4. Tikugwadilani

3. MULUNGU WANTHU MBUYE WATHU Chorus: Alleluia ,Amen (4x) 1. Mulungu wathu Mbuye wathu mama oh! oh! oh! Dzina lanu lalikuli mama oh! oh ! oh Inabuka mbiri yake mama oh ! oh! Oh. Kumwamba ndi pansi ponse.

2. Litchulidwa ndi tiana mama oh! oh ! oh! Takuyamba kulankhula mama oh! oh! oh! Manyazi agwire Anthu mama oh! oh ! oh! Okana kutama Inu mama oh ! oh! oh!

QUITE TIME 1. CHIFUNDO CHA MULUNGU 1. Chifundo cha Mulungu chilibe malire 2. Chikondi cha Mulungu chilibe malire 3. Madalitso a Mulungu

Testimony A prayer to involve the power of the Holy Spirit


SONG TO THE HOLY SPIRIT 1. IDZANI MZIMU WOLENGA 1. Idzani Mzimu wolenga, Mulowe mtima yathu, Ndi kuidzazitsa ndithu Ndi chaulere cha kumwamba 2. Mudza kutisekeretsa, Potininkha moyo wanu, Ndi chikondi chachikulu, Ndi zones zina tisowa 3. Mphatso zanu zozizwitsa, Muziike mmtima mwathu, Zitidziwitse Mulungu, Ndi ntchito zake zokoma.

Teaching time OFFERTORY 1. FANANA NAYE YESU Chorur: Fanana,Fanana,Fanana naye Yesu (2x)
1. 2. 3. 4. Tikamayenda Tikamayimbe Tikamavina Tikamakhala 5. TikamachezaTikamapemphera Tikamakondana TIME FOR PRAYING THE NEEDS OF THE CHURCH Healing Song 1. MULIMPHAVU MWAZI WA YESU 1. Muli mphamvu yodabwitsatu mmwazi wa Yesuyo. Muli mphamvu yodabwitsa mmwazi wa Mwana wa Nkhosa. (2x) 2. Muli moyo wodabwitsatu mmwazi wa Yesuyo. Muli moyo wodabwitsatu mmwazi wa Mwana wa nkhosa. (2x)

2. YESU MUNDICHIRITSE MONGA MENE NDILILI Chorus: A Yesu munafa pamtanda chifukwa cha moyo waga!! 1. Mundichiritse. 2. Mundithandize 3. Munditeteze 4. Mundipulumutse 5. Mundikhululukire THANKS GIVING SONG 1. INU MULULUNGU TITAMA 1. Inu Mulungu titama, Inu ndinudi Ambuye 2. Inu ndinudi Atate, Pa nthawi zones mulipo. 3. Anjelo onse kumwamba Amaimbira inutu 4. Ndinu woyera Mulungu, Mbuye wankhondo kumwamba

Time for Announcements


SONG TO OUR LADY 1. AMAYI ANGA NDI MARIA 1. Amai anga ndi Maria, Amai abwino, okoma, Andisunga,nasamala Nandidziwa,nandikonda 2. Ndine mwana Wa Maria Ndikondanso Amai anga Nditamanda,Ndipemphera Ndipatsatu mtima wanga. 3. Nthawi zones,athangata Ine mwana ndingachimwe, Apemphera,Mlungu Mwana Andipatse chaulere

Closing Prayer...........................

Potrebbero piacerti anche